id int64 2 400 | question_en stringlengths 17 111 | question_ny stringlengths 22 139 | sql_statement stringlengths 48 275 | sql_result stringlengths 6 691 | difficulty_level stringclasses 3
values | table stringclasses 5
values |
|---|---|---|---|---|---|---|
2 | Where was the most rice harvested? | Ndi boma liti komwe anakolola mpunga wambiri? | SELECT district, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE crop = 'Rice'; | [('Karonga', 46385.0)] | easy | production |
3 | Which are the top 5 maize producing districts? | Ndi maboma ati asanu omwe amakolola chimanga chambiri? | SELECT district FROM production WHERE crop = 'Maize' ORDER BY yield DESC LIMIT 5; | [('Lilongwe',), ('Kasungu',), ('Dowa',), ('Mzimba',), ('Mchinji',)] | medium | production |
5 | Which are the top 5 districts that harvested the most tobacco? | Ndi ma boma ati asanu omwe anakolola fodya kwambiri? | SELECT district FROM production WHERE crop = 'Tobacco' ORDER BY yield DESC LIMIT 5; | [('Lilongwe',), ('Dowa',), ('Nkhotakota',), ('Mchinji',), ('Rumphi',)] | medium | production |
6 | Which are the top five districts by soya production? | Ndi ma boma ati asanu omwe anakolola soya kwambiri? | SELECT district FROM production WHERE crop = 'Soy beans' ORDER BY yield DESC LIMIT 5; | [('Lilongwe',), ('Mchinji',), ('Ntchisi',), ('Kasungu',), ('Mzimba',)] | medium | production |
7 | Which district produced more bananas: Lilongwe or Kasungu? | Ndi boma liti lomwe linakolola nthochi zambiri: Lilongwe kapena Kasungu? | SELECT district, SUM(yield) AS Sum_yield FROM production
WHERE crop = 'Bananas'
AND district IN ('Lilongwe', 'Kasungu'); | [('Kasungu', 225545.0)] | hard | production |
9 | What was the yield of apples in dowa? | Ndi ma apulosi ochuluka bwanji omwe anakololedwa ku Dowa mu nyengo yathayi? | SELECT Yield FROM production WHERE District = 'Dowa' AND Crop = 'Apples'; | [(0.0,)] | easy | production |
12 | What was the yield of maize in ntcheu? | Ndi chimanga chochuluka bwanj chidakololedwa ku Ntcheu? | SELECT Yield FROM production WHERE District = 'Ntcheu' AND Crop = 'Maize'; | [(81248.0,)] | easy | production |
13 | Which crop had the highest yield in Ntchisi during 2023-2024? | Ndi mbewu yanji idali ndi zokolola zochuluka ku Ntchisi mu 2023-2024? | SELECT crop, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE district = 'Ntchisi' AND season = '2023-2024'; | [('Maize', 185021.0)] | easy | production |
15 | Which district produced the most Okra in the 2023-2024 season? | Ndi boma liti lidakolola thelele lochuluka mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT District, MAX(Yield) AS Max_Yield FROM production WHERE Crop = 'Okra' AND Season = '2023-2024'; | [('Mulanje', 757.0)] | easy | production |
16 | Which district produced the most Peaches in the 2023-2024 season? | Ndi boma liti lidakolola pichesi ochuluka mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT District, MAX(Yield) AS Max_Yield FROM production WHERE Crop = 'Peaches' AND Season = '2023-2024'; | [('Thyolo', 4179.0)] | easy | production |
17 | Which crop had the highest yield in Nsanje during 2023-2024? | Ndi mbewu yanji idali ndi zokolola zochuluka ku Nsanje mu 2023-2024? | SELECT Crop, MAX(Yield) AS Max_Yield FROM production WHERE District = 'Nsanje' AND Season = '2023-2024'; | [('Sweet potatoes', 145733.0)] | easy | production |
18 | What was the yield of guava in chitipa? | Ndi gwafa ochuluka bwanji adakololedwa ku Chitipa? | SELECT Yield FROM production WHERE District = 'Chitipa' AND Crop = 'Guava'; | [(1337.0,)] | easy | production |
19 | Which district produced the most Avocado pear? | Ndi chigawo chiti chidakolola mapeyala ochuluka kwambili? | SELECT District, MAX(Yield) AS Max_Yield FROM production WHERE Crop = 'Avocado pear'; | [('Thyolo', 26971.0)] | easy | production |
20 | Which crop had the highest yield in Thyolo during 2023-2024? | Ndi mbewu iti idali ndi zokolola zochuluka ku Thyolo mu 2023-2024? | SELECT Crop, MAX(Yield) AS Max_Yield FROM production WHERE District = 'Thyolo' AND Season = '2023-2024'; | [('Sweet potatoes', 454039.0)] | easy | production |
23 | What was the yield of ground beans in ntchisi? | Ndi mzama zochuluka bwanj zidakololedwa ku Ntchisi nyengo ya 2023-2024? | SELECT Yield FROM production WHERE District = 'Ntchisi' AND Crop = 'Ground beans' AND Season = '2023-2024'; | [(224.2,)] | easy | production |
24 | What was the total yield of Paprika in the 2023-2024 season? | Kodi zokolola zonse pamodzi za Paprika zidali zochuluka bwanji mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT SUM(Yield) as Total_Yield FROM production WHERE Crop = 'Paprika' AND Season = '2023-2024'; | [(1047.86,)] | easy | production |
25 | Which crop had the highest yield in Dowa during 2023-2024? | Ndi mbewu iti idali ndi zokolola zambili ku Dowa mu 2023-2024? | SELECT Crop, MAX(Yield) AS Max_Yield FROM production WHERE District = 'Dowa' AND Season = '2023-2024'; | [('Sweet potatoes', 657130.0)] | easy | production |
26 | What was the total yield of Cassava in the 2023-2024 season? | Kodi zokolola zonse pamodzi za chinangwa zidali zochuluka bwanji mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT SUM(Yield) as Total_Yield FROM production WHERE Crop = 'Cassava' AND Season = '2023-2024'; | [(5404033.29,)] | easy | production |
27 | What was total cabbage yield in the country? | Kodi zokolola zonse za kabichi m'dziko muno zinali zochuluka bwanji? | SELECT SUM(Yield) as Total_Yield FROM production WHERE Crop = 'Cabbage'; | [(214782.29,)] | easy | production |
29 | Which district had the highest cotton yield? | Ndi boma liti lomwe linakolola thonje lambiri? | SELECT district, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE crop = 'Cotton'; | [('Nsanje', 4751.0)] | easy | production |
30 | What was the yield of cassava in mangochi? | Ndi chinangwa chochuluka bwanji chidakololedwa ku Mangochi mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT yield FROM production WHERE district = 'Mangochi' AND crop = 'Cassava' AND season = '2023-2024'; | [(0.0,)] | easy | production |
31 | Which crop recorded the highest yield in Kasungu in the 2023-2024 season? | Ndi mbewu iti yomwe inakololedwa mochuluka ku Kasungu mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT crop, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE district = 'Kasungu' AND season = '2023-2024'; | [('Cassava', 597293.0)] | easy | production |
32 | What was the total rice production in the country during the 2023-2024 season? | Kodi mpunga onse pamodzi udakololedwa ochulukwa bwanji mdziko muno mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT SUM(yield) FROM production WHERE crop = 'Rice' AND season = '2023-2024'; | [(138314.762,)] | easy | production |
33 | Which district had the lowest maize yield in the 2023-2024 season? | Ndi boma liti limene lonakolola chimanga chochepa mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT district, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE crop = 'Maize' AND season = '2023-2024'; | [('Lilongwe', 444440.0)] | easy | production |
34 | What was the cassava yield in Salima | Ku Salima anakolola chinangwa chochuluka bwanji? | SELECT yield FROM production WHERE district = 'Salima' AND crop = 'Cassava'; | [(44252.0,)] | easy | production |
35 | Which crop had the highest yield in Mzimba? | Ndi mbewu iti yomwe inali ndi zokolola zambiri ku Mzimba? | SELECT crop, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE district = 'Mzimba'; | [('Cassava', 428043.29)] | easy | production |
36 | What was the yield of groundnuts in dedza? | Ndi mtedza wochuluka bwanji womwe unalimidwa ku Dedza mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT yield FROM production WHERE district = 'Dedza' AND crop = 'Groundnuts' AND season = '2023-2024'; | [(30857.0,)] | easy | production |
37 | Which district produced the most coffee | Ndi boma liti limene linakolola khofi wambiri? | SELECT district, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE crop = 'Coffee'; | [('Chitipa', 7923.0)] | easy | production |
38 | List the top three crops by yield in Karonga for the 2023-2024 season. | Tchulani mbewu zitatu zomwe zinali ndi zokolola zochuluka ku Karonga mu nyengo ya 2023-2024. | SELECT crop FROM production WHERE district = 'Karonga' AND season = '2023-2024' ORDER BY yield DESC LIMIT 3; | [('Cassava',), ('Sweet potatoes',), ('Maize',)] | medium | production |
39 | What was the total tobacco production across all districts in the 2023-2024 season? | Kodi zokolola zonse pamodzi za fodya m'maboma onse zinali zochuluka bwanji mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT SUM(yield) FROM production WHERE crop = 'Tobacco' AND season = '2023-2024'; | [(89616.8275,)] | easy | production |
40 | Which district had higher soybean yield between Kasungu and Lilongwe in the 2023-2024 season? | Pakati pa Kasungu ndi Lilongwe, ndi boma liti lomwe linakolola soya wochuluka mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT district, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE crop = 'Soy beans' AND season = '2023-2024' AND district IN ('Kasungu','Lilongwe'); | [('Lilongwe', 29087.0)] | hard | production |
41 | Which crop had the lowest yield in Mangochi? | Ndi mbewu iti yomwe anakolola zochepa kwambiri ku Mangochi? | SELECT crop, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE district = 'Mangochi'; | [('Mangoes', 150330.0)] | easy | production |
43 | Which districts had maize yields above the national average in the 2023-2024 season? | Ndi ma boma ati anakhalapo ndi chimanga choposa mlingo wadziko lonse pa nthawi ya 2023-2024? | SELECT district FROM production WHERE crop = 'Maize' AND season = '2023-2024' AND yield > (SELECT AVG(yield) FROM production WHERE crop = 'Maize' AND season = '2023-2024'); | [('Dedza',), ('Dowa',), ('Kasungu',), ('Lilongwe',), ('Mchinji',), ('Mzimba',), ('Ntchisi',), ('Zomba',)] | hard | production |
44 | Which crop had the highest total production nationwide in the 2023-2024 season? | Ndi mbewu iti yomwe inali ndi zokolola zochuluka mu nthawi ya 2023-2024? | SELECT crop, SUM(yield) AS Sum_yield FROM production WHERE season = '2023-2024'; | [('Maize', 22780067.78)] | easy | production |
45 | Which district had the second lowest maize yield in the 2023-2024 season? | Ndi boma liti lomwe lili la chiwili limene linali ndi zokolola za chimanga zochepa mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT district FROM production WHERE crop = 'Maize' AND season = '2023-2024' ORDER BY yield ASC LIMIT 1 OFFSET 1; | [('Mwanza',)] | medium | production |
46 | Which crops were produced in all districts during the 2023-2024 season? | Ndi mbewu ziti zomwe zidakololedwa m'maboma onse mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT crop FROM production WHERE season = '2023-2024'GROUP BY crop HAVING COUNT(DISTINCT district) = (SELECT COUNT(DISTINCT district) FROM production WHERE season ='2023-2024'); | [('Apples',), ('Avocado pear',), ('Bananas',), ('Beans',), ('Cabbage',), ('Cassava',), ('Chick peas',), ('Chillies',), ('Coffee',), ('Cotton',), ('Cow peas',), ('Cucumber',), ('Dolichus beans',), ('Egg plants',), ('Field peas',), ('Flue cured',), ('Grams',), ('Grape fruits',), ('Ground beans',), ('Groundnuts',), ('Guav... | hard | production |
48 | How much Cotton in total was harvested in the country? | Ndi thonje lochuluka bwanji lomwe lidakololedwa mdziko muno? | SELECT SUM(Yield) as Total_Yield FROM production WHERE Crop = 'Cotton'; | [(8920.0,)] | easy | production |
49 | Which district had the highest total tomatoes yield across all seasons? | Ndi boma liti lomwe linakolola tomato wochuluka munyengo zonse? | SELECT district, SUM(yield) AS Sum_yield FROM production WHERE crop = 'Tomatoes'; | [('Balaka', 565840.67)] | easy | production |
50 | What was the total soybean production in the 2023-2024 season? | Kodi soya anakololedwa wochuluka bwanji mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT SUM(yield) FROM production WHERE crop = 'Soy beans' AND season = '2023-2024'; | [(179075.525,)] | easy | production |
52 | What was the yield of rice in salima? | Kodi ndi mpunga wochuluka bwanji unakololedwa ku Salima mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT yield FROM production WHERE district = 'Salima' AND crop = 'Rice' AND season = '2023-2024'; | [(9322.0,)] | easy | production |
53 | Which crop had the lowest non-zero yield in Dedza in the 2023-2024 season? | Ndi mbewu iti yomwe inali ndi zokolola zochepetsetsa ku Dedza mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT crop, MAX(yield) AS max_yield FROM production WHERE district = 'Dedza' AND season = '2023-2024' AND yield > 0; | [('Sweet potatoes', 418387.0)] | easy | production |
54 | What is the average maize yield per district in the 2023-2024 season? | Kodi ndi mlingo wapakatikati wanji wa chimanga womwe unakololedwa boma lililonse mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT AVG(yield) FROM production WHERE crop = 'Maize' AND season = '2023-2024'; | [(111128.31975000001,)] | easy | production |
56 | Which districts produced tobacco in the 2023-2024 season? | Ndi maboma ati omwe analima fodya mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT DISTINCT district FROM production WHERE crop = 'Tobacco' AND season = '2023-2024'; | [('Balaka',), ('Blantyre',), ('Chikwawa',), ('Chiradzulu',), ('Chitipa',), ('Dedza',), ('Dowa',), ('Karonga',), ('Kasungu',), ('Likoma',), ('Lilongwe',), ('Machinga',), ('Mangochi',), ('Mchinji',), ('Mulanje',), ('Mzimba',), ('Neno',), ('Nkhata Bay',), ('Nkhotakota',), ('Nsanje',), ('Ntcheu',), ('Ntchisi',), ('Phalombe... | easy | production |
58 | Which district had the highest number of different crops produced in the 2023-2024 season? | Ndi boma liti lomwe linalima mitundu yambili ya mbewu mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT district, COUNT(DISTINCT crop) FROM production WHERE season = '2023-2024' GROUP BY district ORDER BY COUNT(DISTINCT crop) DESC LIMIT 1; | [('Zomba', 46)] | medium | production |
60 | How many districts produced maize in the 2023-2024 season? | Kodi ndi maboma angati omwe analima chimanga mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT COUNT(DISTINCT district) FROM production WHERE crop = 'Maize' AND season = '2023-2024' AND yield > 0; | [(28,)] | medium | production |
61 | What is the average rice yield across all districts in the 2023-2024 season? | Kodi ndi mlingo wapakatikati uti wa zokolola za mpunga m'maboma onse mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT AVG(yield) FROM production WHERE crop = 'Rice' AND season = '2023-2024'; | [(4939.8129285714285,)] | easy | production |
63 | Which crops were produced in Ntcheu during the 2023-2024 season? | Ndi mbewu ziti zomwe zinalimidwa ku Ntcheu mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT DISTINCT crop FROM production WHERE district = 'Ntcheu'AND season ='2023-2024' AND yield > 0; | [('Maize',), ('Beans',), ('Cow peas',), ('Soy beans',), ('Ground beans',), ('Rice',), ('Pigeon peas',), ('Field peas',), ('Wheat',), ('Millet',), ('Sorghum',), ('Groundnuts',), ('Cassava',), ('Sweet potatoes',), ('Tobacco',), ('Cotton',)] | easy | production |
65 | How many different crops were produced nationally in the 2023-2024 season? | Kodi ndi mitundu iti ya mbewu inalimidwa mdziko muno mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT COUNT(DISTINCT crop) FROM production WHERE season = '2023-2024'; | [(46,)] | medium | production |
66 | Which crops had an average yield above 500 in the 2023-2024 season? | Ndi mbewu ziti zomwe zinali ndi zokolola zapakatikati zoposa 500 mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT crop FROM production WHERE season = '2023-2024' GROUP BY crop HAVING AVG(yield) > 500; | [('Apples',), ('Avocado pear',), ('Bananas',), ('Beans',), ('Cabbage',), ('Cassava',), ('Coffee',), ('Cow peas',), ('Cucumber',), ('Egg plants',), ('Flue cured',), ('Groundnuts',), ('Guava',), ('Lemons',), ('Maize',), ('Mangoes',), ('Millet',), ('Onions',), ('Oranges',), ('Pawpaws',), ('Pigeon peas',), ('Pineapples',),... | hard | production |
68 | Which crop showed the largest variation in yield across districts in the 2023-2024 season? | Ndi mbewu iti yomwe inaonetsa kusiyana kwakukulu pa zokolola m'maboma onse mu zaka za 2023-2024? | SELECT crop, (MAX(yield) - MIN(yield)) FROM production WHERE season = '2023-2024' GROUP BY crop ORDER BY (MAX(yield) - MIN(yield)) DESC LIMIT 1; | [('Sweet potatoes', 953323.0)] | medium | production |
70 | How many crops had a total national yield above 1000 in the 2023-2024 season? | Kodi ndi mbewu zingati zomwe zinali ndi zokolola zochuluka zoposa 1000 mdziko muno mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT COUNT(*) FROM (SELECT crop FROM production WHERE season = '2023-2024' GROUP BY crop HAVING SUM(yield) > 1000); | [(43,)] | hard | production |
72 | What is the difference between the highest and lowest rice yields in the 2023-2024 season? | Kodi zokolola za mpunga zochulukitsitsa ndi zochepetsetsa zasiyana mochuluka bwanji mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT MAX(yield) - MIN(yield) FROM production WHERE crop = 'Rice' AND season = '2023-2024'; | [(46385.0,)] | medium | production |
74 | How many districts recorded zero production for sesame in the 2023-2024 season? | Kodi ndi maboma angati omwe sadakolole konse chitowe mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT COUNT(*) FROM production WHERE crop = 'Sesame' AND season = '2023-2024' AND yield = 3; | [(1,)] | easy | production |
75 | Which district had the most balanced crop yields in the 2023-2024 season? | Ndi boma liti lomwe linali ndi zokolola zochukula mofanana mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT district, (MAX(yield) - MIN(yield)) FROM production WHERE season = '2023-2024' GROUP BY district ORDER BY (MAX(yield) - MIN(yield)) ASC LIMIT 1; | [('Likoma', 2242.0)] | medium | production |
76 | What was the average yield of all crops combined in the 2023-2024 season? | Kodi ndi mlingo wapakatikati wotani wa zokolola za mbewu zonse pamodzi mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT AVG(yield) FROM production WHERE season = '2023-2024'; | [(17686.38802950311,)] | easy | production |
79 | What was the total Grape fruits yield in 2023-2024? | Kodi ndi zipatso za mpesa zochuluka bwanji zonse pamodzi zinakololedwa mu nyengo ya 2023-2024? | SELECT SUM(yield) FROM production WHERE crop = 'Grape fruits' AND season = '2023-2024'; | [(239.0,)] | easy | production |
80 | What is the average Chick peas yield? | Ndi mlingo wakatikati womwe anakolola tchana? | SELECT AVG(yield) FROM production WHERE crop = 'Chick peas'; | [(55.357142857142854,)] | easy | production |
83 | How many districts are in the Southern region? | Chigawo chakumwera chili ndi maboma angati? | SELECT COUNT(DISTINCT district_name) FROM population WHERE region_name = 'Southern'; | [(13,)] | medium | population |
84 | List all the distinct Traditional Authorities (TAs) in Phalombe | Lembani m'ndandanda wa mafumu akuluakulu osiyanasiyana omwe ali ku Phalombe | SELECT DISTINCT ta_name FROM population WHERE district_name = 'Phalombe'; | [('TA Mkhumba',), ('TA Jenala',), ('TA Chiwalo',), ('TA Nazombe',), ('TA Nkhulambe',), ('Phalombe Boma',), ('TA Kaduya',), ('Lake Chilwa',)] | easy | population |
85 | How many females in Chikwawa? | Kodi boma la Chikwawa liri ndi akazi angati? | SELECT SUM(population_female) FROM population WHERE district_name = 'Chikwawa'; | [(287794.0,)] | easy | population |
86 | Which districts are in Central region? | Ndi maboma ati omwe ali m'chigawo chapakati? | SELECT DISTINCT district_name FROM population WHERE region_name = 'Central'; | [('Ntchisi',), ('Lilongwe',), ('Salima',), ('Dedza',), ('Kasungu',), ('Mchinji',), ('Nkhotakota',), ('Dowa',), ('Ntcheu',)] | easy | population |
87 | What is the total population in Central region | Kodi chiwerengero cha anthu m'chigawo cha pakati ndichochuluka bwanji? | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE region_name = 'Central'; | [(21215760,)] | easy | population |
88 | How many males are in Nkhotakota? | Ku Nkhotakota kuli amuna angati? | SELECT SUM(population_male) FROM population WHERE district_name = 'Nkhotakota'; | [(192615.0,)] | easy | population |
90 | List all the distinct Traditional Authorities (TAs) in Dowa | Lembani m'ndandanda wa mafumu akuluakulu osiyanasiyana omwe ali ku Dowa | SELECT DISTINCT ta_name FROM population WHERE district_name = 'Dowa'; | [('Dowa Boma',), ('TA Msakambewa',), ('TA Mponela',), ('Mponela Urban',), ('TA Mkukula',), ('TA Dzoole',), ('TA Chiwere',), ('TA Chakhaza',), ('TA Kayembe',)] | easy | population |
91 | List all the distinct Traditional Authorities (TAs) in Mzimba | Lembani m'ndandanda wa mafumu akuluakulu osiyanasiyana omwe ali ku Mzimba | SELECT DISTINCT ta_name FROM population WHERE district_name = 'Mzimba'; | [('TA Mabulabo',), ('STA Levi Jere',), ('TA Mzukuzuku',), ('TA Mzikubola',), ('TA Mtwalo',), ('TA Mpherembe',), ("TA M'Mbelwa",), ('TA Khosolo Gwaza Jere',), ('TA Kampingo Sibande',), ('TA Jaravikuba Munthali',), ('TA Chindi',), ('Mzimba Boma',), ('Vwaza Marsh Reserve',)] | easy | population |
96 | What is the total number of households in Blantyre? | Ndi mabanja ochuluka bwanji omwe ali mu Blantyre? | SELECT SUM(number_households) FROM population WHERE district_name = 'Blantyre'; | [(301630.0,)] | easy | population |
97 | List all the distinct Traditional Authorities (TAs) in Chiradzulu | Lembani m'ndandanda wa mafumu akuluakulu osiyanasiyana omwe ali ku Chiradzulu | SELECT DISTINCT ta_name FROM population WHERE district_name = 'Chiradzulu'; | [('TA Chitera',), ('TA Kadewere',), ('TA Mpama',), ('TA Nchema',), ('STA Sandareki',), ('Chiradzulu Boma',), ('STA Mpunga',), ('STA Onga',), ('TA Likoswe',), ('TA Nkalo',)] | easy | population |
98 | Find the population of Traditional Authority (TA) Area 36. | Pezani chiwerengero cha anthu mudela la mfumu yaikulu 36 | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE ta_name = 'Area 36'; | [(289005,)] | easy | population |
100 | What is the total population in Mangochi? | Chiwerengero cha anthu ku Mangochi ndi chochuluka bwanji? | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE district_name = 'Mangochi'; | [(3348328,)] | easy | population |
101 | How many households in Balaka District? | Ndi mabanja angati omwe ali boma la Balaka? | SELECT SUM(number_households) FROM population WHERE district_name = 'Balaka'; | [(101574.0,)] | easy | population |
103 | Find the population of Traditional Authority (TA) Area 13? | Pezani chiwerengero cha anthu mudela la mfumu yaikulu 13 | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE ta_name = 'Area 13'; | [(3,)] | easy | population |
104 | Which Traditional Authority (TA) in Chiradzulu has the largest total population? | Kodi ndi mfumu yaikulu iti yomwe ili ndi chiwerengero cha anthu chokwera boma la Chiradzulu? | SELECT ta_name, SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) as total_pop FROM population WHERE district_name = 'Chiradzulu' GROUP BY ta_name ORDER BY total_pop DESC LIMIT 1; | [('TA Likoswe', 199343)] | medium | population |
105 | Find the total count of districts in Northern region | Welengani ma boma onse omwe ali chigawo chaku mpoto | SELECT COUNT(DISTINCT district_name) FROM population WHERE region_name = 'Northern'; | [(7,)] | medium | population |
106 | How many females are in Balaka? | Ndi akazi angati ali ku Balaka? | SELECT SUM(population_female) FROM population WHERE district_name = 'Balaka'; | [(229105.0,)] | easy | population |
107 | What is the total population in Dowa? | Chiwerengero cha anthu m'boma la Dowa ndo chochuluka bwanji? | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE district_name = 'Dowa'; | [(2189187,)] | easy | population |
108 | How many females are in Chitipa? | Ndi akazi angati ali ku Chitipa? | SELECT SUM(population_female) FROM population WHERE district_name = 'Chitipa'; | [(120535.0,)] | easy | population |
109 | Find the population of Traditional Authority (TA) Area 25. | Pezani chiwerengero cha anthu okhala m'dela la mfumu yaikulu 25 | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE ta_name = 'Area 25'; | [(289170,)] | easy | population |
110 | What is the total population in Chitipa? | Chiwerengero cha anthu ku Chitipa ndi chochuluka bwanji? | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE district_name = 'Chitipa'; | [(663660,)] | easy | population |
111 | List all the distinct Traditional Authorities (TAs) in Chitipa | Lembani m'ndandanda wa mafumu akuluakulu osiyanasiyana omwe ali ku Chitipa | SELECT DISTINCT ta_name FROM population WHERE district_name = 'Chitipa'; | [('TA Mwenemisuku',), ('TA Nthalire',), ('STA Nthengatenga',), ('TA Mwenewenya',), ('STA Lwangwa',), ('STA Wavikaza',), ('Chitipa Boma',), ('TA Kameme',), ('Nyika Ntational Park-Chitipa',), ('STA Bulambya Songwe',), ('TA Mwabulambya',)] | easy | population |
112 | How many females are in Thyolo? | Ndi akazi angati ali ku Thyolo? | SELECT SUM(population_female) FROM population WHERE district_name = 'Thyolo'; | [(380697.0,)] | easy | population |
113 | Which Traditional Authority (TA) in Blantyre has the largest total population? | Kodi ndi mfumu yaikulu iti yomwe ili ndi chiwerengero cha anthu chochuluka kwambli ku Blantyre? | SELECT ta_name, SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) as total_pop FROM population WHERE district_name = 'Blantyre' GROUP BY ta_name ORDER BY total_pop DESC LIMIT 1; | [('TA Kapeni', 270899)] | medium | population |
114 | List all the distinct Traditional Authorities (TAs) in Blantyre city | Lembani m'ndandanda wamafumu akuluakulu osiyanasiyana mu mzinda wa Blantyre | SELECT DISTINCT ta_name FROM population WHERE district_name = 'Blantyre'; | [('TA Kapeni',), ('TA Lundu',), ('TA Chigaru',), ('TA Makata',), ('TA Machinjiri',), ('Chilomoni Ward',), ('Michiru Ward',), ('Nyambadwe Ward',), ('Mbayani Ward',), ('South Lunzu Ward',), ('Mapanga Ward',), ('Green Corner Ward',), ('Misesa Ward',), ('Ndirande Gamulani Ward',), ('Ndirande Makata Ward',), ('Soche West Wa... | easy | population |
116 | What is the population of Traditional Authority (TA) Area 31? | Kodi chiwerengero cha anthu m'dera la mfumu yayikulu 36 ndi chochuluka bwanji? | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE ta_name = 'Area 31'; | [(0,)] | easy | population |
117 | How many females are in Karonga? | Ndi akazi angati ali ku Karonga? | SELECT SUM(population_female) FROM population WHERE district_name = 'Karonga'; | [(188831.0,)] | easy | population |
119 | Which Traditional Authority (TA) in Chikwawa has the largest number of households? | Ndi mfumu yaikulu iti ku Chikwawa yomwe ili ndi mabanja ochuluka kwambiri? | SELECT ta_name, SUM(number_households) as total_hh FROM population WHERE district_name = 'Chikwawa' GROUP BY ta_name ORDER BY total_hh DESC LIMIT 1; | [('TA Ngabu', 33888.0)] | medium | population |
120 | Find the total population in Southern region | Pezani kuchuluka kwa anthu onse okhala m'chigawo chakumwela | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE region_name = 'Southern'; | [(21757131,)] | easy | population |
121 | How many males are in Mchinji? | Ku Mchinji kuli amuna angati? | SELECT SUM(population_male) FROM population WHERE district_name = 'Mchinji'; | [(296786.0,)] | easy | population |
122 | Which Traditional Authority (TA) in Blantyre has the largest number of households? | Ndi mfumu yayikulu iti yomwe ili ndi mabanja ambiri ku Blantyre? | SELECT ta_name, SUM(CAST(number_households AS INTEGER)) as total_hh FROM population WHERE district_name = 'Blantyre' GROUP BY ta_name ORDER BY total_hh DESC LIMIT 1; | [('TA Kapeni', 25440)] | medium | population |
123 | How many males in Chikwawa district? | Ndi amuna angati omwe ali ku Chikwawa? | SELECT SUM(population_male) FROM population WHERE district_name = 'Chikwawa'; | [(276890.0,)] | easy | population |
124 | Which Traditional Authority (TA) in Chiradzulu has the largest number of households? | Ndi mfumu yayikulu iti ku Chiradzulu yomwe ili ndi mabanja ambiri? | SELECT ta_name, SUM(CAST(number_households AS INTEGER)) as total_hh FROM population WHERE district_name = 'Chiradzulu' GROUP BY ta_name ORDER BY total_hh DESC LIMIT 1; | [('TA Likoswe', 17392)] | medium | population |
125 | Which districts are in Northern region? | Ndi maboma ati omwe ali mchigawo chakumpoto? | SELECT DISTINCT district_name FROM population WHERE region_name = 'Northern'; | [('Mzimba',), ('Likoma',), ('Chitipa',), ('Karonga',), ('Nkhata Bay',), ('Rumphi',), ('Mzuzu',)] | easy | population |
126 | List all the distinct Traditional Authorities (TAs) in Karonga | Pelekani ndandanda wa mafumu akuluakulu osiyanasiyana ku Karonga | SELECT DISTINCT ta_name FROM population WHERE district_name = 'Karonga'; | [('TA Wasambo',), ("TA Mwirang'ombe",), ('TA Mwakaboko',), ('TA Kyungu',), ('TA Kilupula',), ('Karonga Town',), ('Nyika National Park-Karonga',)] | easy | population |
128 | How many males in Chiradzulu? | Ku Chiradzulu kuli amuna angati ? | SELECT SUM(population_male) FROM population WHERE district_name = 'Chiradzulu'; | [(169679.0,)] | easy | population |
130 | Which Traditional Authority (TA) in Chikwawa has the largest male population? | Ndi mfumu yayikulu iti ku Chikwawa yomwe ili ndi chiwerengero cha anthu chochuluka? | SELECT ta_name, SUM(CAST(population_male AS INTEGER)) as total_male FROM population WHERE district_name = 'Chikwawa' GROUP BY ta_name ORDER BY total_male DESC LIMIT 1; | [('TA Ngabu', 77120)] | medium | population |
133 | List all the distinct Traditional Authorities (TAs) in Dedza | Ku Dedza kuli mafumu akuluakulu osiyanasiyana angati? | SELECT DISTINCT ta_name FROM population WHERE district_name = 'Dedza'; | [('TA Tambala',), ('TA Kasumbu',), ('TA Kaphuka',), ('TA Kachere',), ('TA Chilikumwendo',), ('TA Chauma',), ('TA Kamenya Gwaza',), ('TA Kachindamoto',), ('Dedza Boma',)] | easy | population |
134 | How many households are in Likoma? | Ku Likoma kuli mabanja angati? | SELECT SUM(number_households) FROM population WHERE district_name = 'Likoma'; | [(2892.0,)] | easy | population |
135 | What is the population of Traditional Authority (TA) Area 35? | Chiwerengero cha anthu mdera la mfumu yayikulu 35 ndi chochuluka bwanji? | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE ta_name = 'Area 35'; | [(44546,)] | easy | population |
136 | What is the total population in Likoma? | Ku Likoma kuli chiwerengero cha anthu chochuluka bwanji? | SELECT SUM(CAST(total_population AS INTEGER)) FROM population WHERE district_name = 'Likoma'; | [(14527,)] | easy | population |
137 | How many Traditional Authorities (TAs) are in Mulanje? | Ku Mulanje kuli mafumu akuluakulu angati? | SELECT COUNT(DISTINCT ta_name) FROM population WHERE district_name = 'Mulanje'; | [(10,)] | medium | population |
138 | How many Traditional Authorities (TAs) are in Chikwawa? | Ku Mulanje kuli mafumu akuluakulu angati? | SELECT COUNT(DISTINCT ta_name) FROM population WHERE district_name = 'Chikwawa'; | [(15,)] | medium | population |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.