Dataset Viewer
Auto-converted to Parquet Duplicate
score
float32
1.04
1.25
Chichewa
stringlengths
10
500
Swahili
stringlengths
4
500
1.249855
Atumiki anga anadzatsandzaya, mbwenye imwe munadzatsukwala.
Watumishi wangu watashangilia, lakini ninyi mtaona aibu.
1.249832
M'malo mwake iwo anati: "Kodi tichite chiyani pamenepa, chifukwa munthu uyu [Yesu] akuchita zizindikiro zochuluka?"
Badala yake, walisema: "Tufanye nini, kwa sababu mtu huyu [Yesu] anafanya ishara nyingi?"
1.249654
"Anthu 5 omwe mudzakumane nawo kumwamba."
"Watu 5 ambao utakutana nao mbinguni."
1.249593
""Ndipo m'bale wanga (Haaruni) ndikatswiri pakuyankhula kuposa ine.
Na ndugu yangu, Harun, ni fasihi zaidi ulimi wake kuliko mimi.
1.249571
Kodi ndimafuna nditakhala munthu wamakhalidwe otani? - Akolose 3:10.
Ninataka kuwa mtu wa aina gani? - Wakolosai 3:10.
1.249319
Yankhani mafunso awa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m'Baibulo omwe akusowapo.
Jibu maswali haya, na utaje mistari ya Biblia ambayo haijaonyeshwa.
1.249294
Kodi Mukulandira "Chakudya pa Nthawi Yoyenera?"
Unapata Chakula "kwa Wakati Unaofaa"?
1.249199
Izi ndi zimene mayi wina wa ku Japan ankachita pophunzitsa ana ake awiri.
Mama mmoja nchini Japani alifanya hivyo.
1.248969
Atumiki anga adzamwa, koma inuyo mudzakhala ndi ludzu.
Watumishi wangu watakunywa, lakini ninyi mtakuwa na kiu.
1.248965
Inu ndi amene muli ndi mawu amoyo wosatha."
Wewe una maneno ya uzima wa milele."
1.248898
Kodi Mukulandira "Chakudya pa Nthawi Yoyenera?"
Je, Unapata 'Chakula kwa Wakati Unaofaa'?
1.248825
Koyamba kumva Taiwan?
Mara ya kwanza kusikia Taiwan?
1.248781
Ndithu ine ndikukuonani inu ndi anthu anu kuti muli m'kusokera koonekera."
Hakika mimi nakuona wewe na watu wako mmo katika opotofu ulio wazi. ***
1.248688
Perekani zitsanzo za m'Malemba zosonyeza kuti kawirikawiri sizinali zophweka kwa atumiki okhulupirika a Mulungu kuchita chifuniro chake.
Toa vielelezo vya Kimaandiko kuonyesha kwamba haikuwa rahisi sikuzote kwa watumishi waaminifu wa Mungu kufanya mapenzi yake.
1.248676
Cidzindikiro cinafuna kudza kaona imwe ndi ici: Munagumana mwana wa kumala kumbulunganyiwa na nguwo, mbagoneswa m'mwadiya wakudyera pifuyo."
Na hii ndiyo ishara kwenu: Mtamkuta mtoto aliyefungwa kwa vitambaa akiwa amelala katika hori."
1.248532
Ndakhalapo Chenjerani ndi Google kwakanthawi!
nimekuwa jihadharini na Google kwa muda!
1.248518
Potero, Mfumu Agripa, sindinakhala ine wosamvera masomphenya a Kumwamba;
Kwa hiyo, Ee Mfalme Agripa, sikuyaasi yale maono ya mbinguni,
1.248476
Mwana wa Munthu adzabwera mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo ake, ndipo pomwepo mphoto kwa munthu aliyense monga mwa ntchito zake.
Kwa sababu Mwana wa Adamu atakuja katika utukufu wa Baba yake pamoja na malaika zake; ndipo atakapomlipa kila mtu kwa kadiri ya matendo yake.
1.24842
Iye ankakhulupirira kuuka kwa akufa.
Aliamini ufufuo.
1.248291
Kodi Ine ndisamwere chikho chimene Atate andipatsa?"
Je, hainipasi kukinywea kikombe alichonipa Baba?"
1.24819
Choncho mipingo inapitiriza kulimba m'chikhulupiriro ndipo chiwerengero chinapitiriza kuwonjezeka tsiku ndi tsiku."
Kwa hiyo, kwa kweli, makutaniko yakaendelea kufanywa imara katika imani na kuongezeka hesabu siku baada ya siku."
1.248132
Kodi si ndiwe ndi nyumba yonse ya abambo ako?"
Siyo kwako na nyumba ya baba yako yote?"
1.24812
Kodi masiku ano odzozedwa asonyeza bwanji kuti ndi 'anthu odziwika ndi dzina la Yehova'?
Watiwa-mafuta wameonyeshaje kwamba wao ndio "watu kwa ajili ya jina [la Yehova]" leo?
1.24784
Esther ankandithandizanso mu utumiki.
Esther alinisaidia pia katika huduma.
1.247636
Kodi ndingamutsatire bwanji mosamalitsa?'
Ninaweza kumfuata jinsi gani kwa ukaribu zaidi?'
1.247303
• Kodi panopa ndikumamwa mowa kwambiri kuposa kale?
• Je, ninakunywa pombe kali sasa kuliko hapo awali?
1.247182
"Mtendere ukhale pa Nuh pa zolengedwa zonse.
Iwe salama kwa Nuhu ulimwenguni kote!
1.247104
Limati: "Yehova ali pafupi ndi onse oitanira pa iye.
Inasema hivi: "Yehova yuko karibu na wote wanaomwitia, wote wanaomwitia yeye katika ukweli.
1.247056
Sitingathe kudziwa zonse zomwe angelo akuchita panopo.
Hatuwezi kujua mambo yote ambayo malaika wanafanya leo.
1.247026
Olambira Oona Amadziwika ndi Zipatsa Zawo
Waabudu wa Kweli Wanatambuliwa kwa Matunda Yao
1.247002
Adzagonera ndani m'phiri lanu lopatulika?"
Ni nani atakayekaa katika mlima wako mtakatifu?"
1.246804
Kodi muli ndi funso lina kwa Jack?
Je, unayo swali jingine kwa Jack?
1.246714
Tathandiza anthu zikwi monga inu!
Tumewasaidia maelfu ya watu kama wewe!
1.24661
M'bale wina analemba kuti: "Ndimathokoza kwambiri makolo anga chifukwa anandilera bwino.
Ndugu mmoja aliandika hivi: "Ninashukuru sana jinsi wazazi wangu walivyonilea.
1.246323
19 Pakuti kuyenera kuti pakhale mipatuko mwa inu, kuti iwo wobvomerezedwa awonetsedwe pakati pa inu.
maana ni lazima fikira tofauti ziweko miongoni mwenu, ili wale walio thabiti wapate kutambulikana.
1.24632
"Adati: "Tamkhulupirira Mbuye wa zolengedwa."
Wakasema: Tumemuamini Mola Mlezi wa viumbe vyote, ***
1.246239
Ndipo ndithu tsiku limodzi kwa Mbuye wako lili ngati zaka chikwi chimodzi mukawerengedwe kanu.
Nahakika siku moja kwa Mola wako Mlezi ni kama miakaelfu mnavyo hisabu nyinyi.
1.246033
Kotero kuti anaposa angelo monga dzina limene analilandira ndiloposa iwo.
Kwa hivyo alikua bora kuliko malaika kama vile jina alilorithi ni bora kupita yao.
1.24565
Inu muli nawo mawu a moyo wosatha."
Wewe una maneno ya uzima wa milele."
1.24512
Pakuti Mulungu ndi wamkulu kuposa mitima yathu ndipo Iye amadziwa zonse.
Kwa maana Mungu ni mkuu kuliko mioyo yetu, naye anajua kila kitu.
1.245032
37 Ine ndisadziwa kuti ndimwe a dzindza ya Abharaamu, mbwenye musasaka kundipha, thangwi fala yanga nkhabe pita muna imwe.
"Najua ya kuwa ninyi ni uzao wa Ibrahimu lakini mnatafuta kuniua kwa sababu neno langu halimo ndani yenu.
1.244929
Atatuwa anali ana a Nowa, ndipo Kuchokera pamenepa anthu onse padziko lapansi anafalikira."
Hawa watatu walikuwa wana wa Noa, na kutoka kwao ndio watu wote wa dunia walienea kotekote. "
1.244915
mwandisandutsa kukhala mtsogoleri wa anthu a mitundu ina.
umenifanya kuwa kiongozi wa mataifa,
1.244841
kapenanso kuti anthu adzati, 'Uwu uli apa,' kapena 'Uwo uli apo,' Pakuti taonani ufumu wa Mulungu uli pakati panu."
wala hawatasema, Tazama, upo huku, au, kule, kwa maana, tazama, ufalme wa Mungu umo ndani yenu.
1.24481
Ndalama zimenezi uzipereke kwa Aaroni ndi ana ake aamuna kuti ukhale mtengo woombolera Aisraeli woonjezerawo."
Nawe utawapa Haruni na wanawe hao Walawi wawe nao; amepewa watu hao kabisa kwa ajili ya wana wa Israeli.
1.244768
Yendanibe ngati ana a kuwala."
Endeleeni kutembea kama watoto wa nuru."
1.244705
Roger ali ndi ake blog yanu, nanunso!
Roger ana yake blog mwenyewe, pia!
1.244622
USP yanu ingakhalenso (ndipo iyenso ikhale!)
USP yako pia inaweza (na inapaswa kuwa pia!)
1.244471
(Iwo akhala akuchita bizinesi kuyambira 2005...)
(Wamekuwa wakifanya biashara tangu 2005...)
1.244389
Watseka maso anu, inu aneneri;
Ameziba macho yenu (ninyi manabii);
1.244086
Iye analemba kuti: "Tamverani abale anga okondedwa.
Aliandika hivi: "Sikilizeni, ndugu zangu wapendwa.
1.244023
musadandaula, monga ena a iwo anadandaula, naonongeka ndi woonongayo.
Wala msinung'unike kama baadhi yao walivyonung'unika, wakaangamizwa na Mwangamizi!
1.243952
Mwana wa Munthu adzabwera mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo ake, ndipo pomwepo mphoto kwa munthu aliyense monga mwa ntchito zake.
Kwa sababu Mwana wa Adamu atakuja katika utukufu wa Baba yake pamoja na malaika zake; ndipo atakapomlipa kila mtu kwa kadiri ya matendo yake."
1.243826
Atsikana ochokera konsekonse padziko lapansi akuyembekezerani kale!
Wasichana kutoka kote ulimwenguni tayari wanakusubiri!
1.243807
"Ndimibadwo ingati imene tidaiononga pambuyo pa Nuh!
[17.17] Na kaumu ngapi tumeziangamiza baada ya Nuhu!
1.24374
Koma Mulungu ndi wosiyana ndi anthu chifukwa iye amadziwa mfundo zonse.
Tofauti na wanadamu, Mungu anajua mambo yote ya hakika.
1.243715
Sindikufanana ndi Mose, Gideoni, kapena Davide.'
Bila shaka siwezi kuwa kama Musa, Gideoni, au Daudi.'
1.24335
Mabuku athu asindikizidwa ku Pakistan!
Vitabu vyetu vimechapishwa nchini Pakistan!
1.24327
Atatu awa ndiwo ana a Nowa, ndi kwa iwo ndi aliyense mu dziko anayala. "
Hawa watatu walikuwa wana wa Nuhu na kwa hao nchi yote ikaenea watu.
1.24308
Kukhulupirira Mulungu Amene Mwina Sitikum'dziŵa
Kumwamini Mungu Ambaye Huenda Hatumjui
1.243028
Kodi Akhristu oona anasonyeza bwanji kuti anali 'anthu odziwika ndi dzina la Yehova'?
Wakristo wa kweli wangeonyeshaje kwamba wao ni "watu kwa ajili ya jina [la Yehova]"?
1.243023
Iwo anali olemera chifukwa anali ndi chikhulupiriro ndiponso anali okhulupirika kwa Mulungu.
Walikuwa matajiri kwa sababu ya imani na utimilifu wao kwa Mungu.
1.243003
Ndipo palibe chilichonse chimene mbuye wanga sanachipereke kwa ine kupatula inuyo, chifukwa ndinu mkazi wake.
Bwana wangu hakunizuilia kitu cho chote isipokuwa wewe, kwa kuwa wewe ni mke wake.
1.243002
Ine ndi Ferdinand tinali ndi nkhani zambiri zoti tiuzane!
Mimi na Ferdinand tulikuwa na mambo mengi sana ya kuambiana!
1.242977
Kuchokera kwa ana awo kapena kwa anthu achilendo?"
Je, ni kutoka kwa watoto wao au kutoka kwa watu wengine?"
1.242409
Ndithu amithenga athu (angelo) akulemba ziwembu zanu (zonse) zimene mukuchita.
Hakika wajumbe wetu wanayaandika mnayo yapanga.
1.241828
"Mtheradi tidzawafunsa (anthu) amene anatumiziridwa (atumiki), naonso atumikiwo tidzawafunsa.
Na kwa yakini tutawauliza wale walio pelekewa Ujumbe, na pia tutawauliza hao
1.241797
Rom 10:12 Pakuti kulibe kusiyana Myuda ndi Mhelene; pakuti yemweyo ali Ambuye wa onse, nawachitira zolemera onse amene ayitana pa Iye;
Jambo hili ni kwa wote, kwani hakuna tofauti kati ya Wayahudi na wasio Wayahudi; Bwana wa wote ni mmoja, naye ni mkarimu sana kwao wote wamwombao.
1.241797
Rom 10:12 Pakuti kulibe kusiyana Myuda ndi Mhelene; pakuti yemweyo ali Ambuye wa onse, nawachitira zolemera onse amene ayitana pa Iye;
jambo hili ni kwa wote, kwani hakuna tofauti kati ya wayahudi na wasio wayahudi; bwana wa wote ni mmoja, naye ni mkarimu sana kwao wote wamwombao.
1.241781
Ndakhala ndi nkhawa zofananazo, Leonardo.
Nimekuwa na wasiwasi kama huo, Leonardo.
1.2416
Pakuti dzanja lanu linali kundilemera usana ndi usiku."
Kwa maana usiku na mchana mkono wako ulinilemea."
1.241252
Act 15:9 Ndipo sadalekanitsa ife ndi iwo, nayeretsa mitima yawo m'chikhulupiriro.
15:9 Hakufanya ubaguzi wowote kati yetu na wao; aliitakasa mioyo yao kwa imani.
1.241029
7"Kodi ndiwe munthu woyamba kubadwa?
7 "Je, wewe ni mtu wa kwanza kuzaliwa?
1.240792
Kwa zaka 40 munawapatsa chakudya . . .
Kwa miaka 40 ukawapa chakula . . .
1.240731
Iye anabwera ndipo analalikira mtendere kwa inu amene munali kutali ndi mtendere ndiponso kwa iwonso amene anali pafupi.
Akaja akahubiri amani kwenu ninyi mliokuwa mbali, na amani kwao wale waliokuwa karibu."
1.240713
Kodi "Adamu womalizira" adzathandiza bwanji akufa?
"Adamu wa mwisho" atawasaidiaje wafu?
1.24065
Ndithu Ife tidawalenga kuchokera m'zimene akudziwa (madzi opanda pake).
Hakika Sisi tumewaumba kutokana na wanachokijua.
1.240586
Kodi iweyo unayamba wanama? - * Ngakhale akuluakulu ena amene amakonda Mulungu ananamapo.
Je, umewahi kudanganya? - * Hata baadhi ya watu wazima wanaompenda Mungu wamewahi kudanganya.
1.240497
Pakuti mkwiyo wake tsiku lalikulu wabwera, ndipo amene angaime?
Maana siku maalum ya ghadhabu yao imefika, na ambaye anaweza kusimama?
1.24033
Kumbukirani kuti atatu a iwo adzasungidwa.
Kumbuka kwamba tatu kati yao zitahifadhiwa.
1.240191
"Koma tawabweretsera choonadi; ndithu iwo ngabodza (potsutsana ndi choonadicho).
Bali tumewaletea Haki, na kwa hakika wao ni waongo.
1.240032
Ndipotu, mu chaputala 4, ndinakuphunzitsani momwe mungachitire.
Kwa kweli, katika sura ya 4, nilikufundisha jinsi ya kufanya hivyo.
1.239987
Iye anadziŵa kuti sinali nthaŵi yomwe Mulungu analinganiza kudzachita zimenezo.
Alijua kuwa wakati wa Mungu wa kufanya hivyo haukuwa umefika.
1.239944
Koma Mulungu ndi wosiyana ndi anthu chifukwa iye amadziwa mfundo zonse.
Tofauti na wanadamu, Mungu anajua mambo yote.
1.239854
Iye anati: "Chifukwa chake dikirani; chifukwa simudziwa tsiku limene Ambuye wanu adzabwera ...
Basi, kesheni, kwa maana hamjui siku atakayokuja Bwana wenu.
1.23981
Sipadzakhala pulogalamu yamasana.
Hakutakuwa na kipindi cha alasiri.
1.239631
• Ndi ntchito yaikulu iti yophunzitsa yomwe idzachitika m'dziko latsopano?
• Ni kazi gani kubwa ya kufundisha itakayofanywa katika ulimwengu mpya?
1.239562
26Zidzatha izi, koma Inu mukhala: Inde, zidzatha zonse ngati cabvala;
Hizo zitatoweka, lakini wewe wabaki daima, zote zitachakaa kama vazi.
1.239408
Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje, ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a nyanja.
Ndipo amani yako ingekuwa kama mto, na uadilifu wako kama mawimbi ya bahari."
1.239366
Limeneli ndilo lamulo lalikulu kwambiri komanso loyamba." - Mat.
Hii ndiyo amri iliyo kubwa na ya kwanza." - Mt.
1.238919
Kodi mungatewezere tani ciratizo ca Zuze penu winango ankukucitirani bzinthu mwakusaya cirungamo?
Unaweza kuigaje mfano wa Yosefu wengine wanapokutendea isivyo haki?
1.238633
(Inde, ndikudziwa kuti ndakalamba!)
(Ndio, najua mimi ni mzee!)
1.238558
Kodi iye sadadziwe kuti Allah adawaononga anthu patsogolo pake omwe adali anyonga kwambiri kuposa iye, komanso osonkhanitsa chuma chambiri?
Je, hakujua kwamba Mwenyezi Mungu amekwishaangamiza karne zilizokuwa kabla yake waliokuwa na nguvu zaidi kuliko yeye na wenye makundi makubwa zaidi.
1.238512
16 Davide ndi chitsanzo kwa makolo masiku ano.
16 Daudi ni mfano kwa wazazi leo.
1.238365
Pakuti ici ndi cikondi ca Mulungu, kuti tisunge malamulo ace: ndipo malamulo ace sali olemetsa.
Kwa maana huku ndiko kumpenda Mungu, kwamba tuzishike amri zake; wala amri zake si nzito.
1.238346
Ife tisalambira cinadziwa ife, thangwi kupulumuswa kwabuluka kuna madjuda.
Ninyi Wasamaria mnamwabudu yule msiyemjua, lakini sisi tunamjua huyo tunayemwabudu, kwa maana wokovu unatoka kwa Wayahudi.
1.238334
Ndinatengeredwa ku khoti maulendo 17.
Nilifikishwa mahakamani mara 17.
1.238275
Ndiyeno akuti kwa ophunzira ake: "Tiyeni tipitenso ku Yudeya."
Kisha akawaambia wanafunzi wake, "Twendeni tena Yudea!."
1.238223
17 Zimene Mariya ankalankhula.
17 Mambo yenye Maria alisema.
1.238149
Mwachitsanzo, m'chaputala 4 anafotokoza za Abulahamu.
Katika sura ya 4, alizungumza kuhusu Abrahamu.
End of preview. Expand in Data Studio

Chichewa-Swahili_Sentence-Pairs Dataset

This dataset contains sentence pairs for African languages along with similarity scores. It can be used for machine translation, sentence alignment, or other natural language processing tasks.

This dataset is based on the NLLBv1 dataset, published on OPUS under an open-source initiative led by META. You can find more information here: OPUS - NLLB-v1

Metadata

  • File Name: Chichewa-Swahili_Sentence-Pairs
  • Number of Rows: 1078600
  • Number of Columns: 3
  • Columns: score, Chichewa, Swahili

Dataset Description

The dataset contains sentence pairs in African languages with an associated similarity score. Each row consists of three columns:

  1. score: The similarity score between the two sentences (range from 0 to 1).
  2. Chichewa: The first sentence in the pair (language 1).
  3. Swahili: The second sentence in the pair (language 2).

This dataset is intended for use in training and evaluating machine learning models for tasks like translation, sentence similarity, and cross-lingual transfer learning.

References

Below are papers related to how the data was collected and used in various multilingual and cross-lingual applications:

[1] Holger Schwenk and Matthijs Douze, Learning Joint Multilingual Sentence Representations with Neural Machine Translation, ACL workshop on Representation Learning for NLP, 2017

[2] Holger Schwenk and Xian Li, A Corpus for Multilingual Document Classification in Eight Languages, LREC, pages 3548-3551, 2018.

[3] Holger Schwenk, Filtering and Mining Parallel Data in a Joint Multilingual Space ACL, July 2018

[4] Alexis Conneau, Guillaume Lample, Ruty Rinott, Adina Williams, Samuel R. Bowman, Holger Schwenk and Veselin Stoyanov, XNLI: Cross-lingual Sentence Understanding through Inference, EMNLP, 2018.

[5] Mikel Artetxe and Holger Schwenk, Margin-based Parallel Corpus Mining with Multilingual Sentence Embeddings arXiv, Nov 3 2018.

[6] Mikel Artetxe and Holger Schwenk, Massively Multilingual Sentence Embeddings for Zero-Shot Cross-Lingual Transfer and Beyond arXiv, Dec 26 2018.

[7] Holger Schwenk, Vishrav Chaudhary, Shuo Sun, Hongyu Gong and Paco Guzman, WikiMatrix: Mining 135M Parallel Sentences in 1620 Language Pairs from Wikipedia arXiv, July 11 2019.

[8] Holger Schwenk, Guillaume Wenzek, Sergey Edunov, Edouard Grave and Armand Joulin CCMatrix: Mining Billions of High-Quality Parallel Sentences on the WEB

[9] Paul-Ambroise Duquenne, Hongyu Gong, Holger Schwenk, Multimodal and Multilingual Embeddings for Large-Scale Speech Mining, NeurIPS 2021, pages 15748-15761.

[10] Kevin Heffernan, Onur Celebi, and Holger Schwenk, Bitext Mining Using Distilled Sentence Representations for Low-Resource Languages

Downloads last month
14

Collection including michsethowusu/chichewa-swahili_sentence-pairs